» » » Ngati Mzimbe Lyrics

Ngati Mzimbe Lyrics

Name Taken - Hold On For Your Dearest Life Lyrics

Ngati Mzimbe by Trap Squad




Ngati Mzimbe
Intro [Revolver]
Trap squad aise
Royal fam
Yeah
Verse 1 [revolver]
Zimakoma kumathelo ngati bus ya kwa jali
Nkhawa utapanga burry ngati braz ya patali
Chapatali timakhala ngati tapenga
Mkazi wanga wa mmaloto uja ndampeza
Akandinong'oneza zam'dziko ndimapanga mute
Amvekele my crooked smile is kinda cute
Unali kuti moyo wanga wonseu
You make a G turn soft when you say you-gotta go
Ati kwada is the reason
Ndinamuwuza usapite ngati chisoni
Baby you're the cure to my disease
Mtima wanga umandipweteka when you leave
Gave you my heart do with it as you please
I wish I could take this moment and freeze
Usakaike ndiwe wanga basi
Ndikamatchila ndi iwe zimakhala ngati
Mzimbe
Chorus [sir patricks, stich fray]
Ngati mzimbe ukomela ku msinde
Ngati tulo likoma ku mbanda kucha
Tikamacheza usapite honey usapite
Tikamacheza ngati usapite honey usapite tizicheza
Verse 2 [Chavura]
Sweet ndingofila bho man
Ndavaya kwao wandishophela ka yogurt
Which ndingomwela stroll man
Wa awuza ana panja kuti chokani
Muti sokoneza
Muti phokosela Ndamugwila nkhosi easy kumunong'oneza
Wandipasa kiss ngati barabas
Mkazi uyu ine ndimupasa mwana basi
Mkulu wina anamdyesa nazo nyani
Atakomedwa kutchatisa ka mkazi
Anachita kufasa kukombezela msuzi
Osadziwa kuti akudya barboon
Me anandiuza I love you
Ndakuphikila zokoma iwe top goon
Nnamupasa kaye mphaka alawe portion
Sukudziwa mwina mfana wathila poison
(back to chorus)
Verse 3
[sir patricks]
Umalasa mtima ukatulukila
Ukati honey ndabwela kuzakuphikila
Pachisoni kachikondi amazembelera
Poti ndimadziwa wabwela za temporaly posachedwa usanzika
[stich fray]
Mutu wanga umazungulira
Zimandivuta mtimawu kuwugwila ine
Ndikakuona iwe ukupita
Mu mtima mumawawa mutu umawawa
Kuganizila zina
Sizitheka ndipo sindimaona mdima
Tingokwatila mwina
Its hard to watch you go ndipo zili ngati mzimbe





Copyright statement DMCA « Lyrics are property and copyright of their owners. Song provided for educational and language learning purposes